Tsopano tikupeleka maphunziro a Baibulo pa intaneti mwaulere kwathunthu. M'maphuziro afupiafupi khumi ndi asanu muphunzira zambiri za Yesu.